Umaopa Zingati?

K1-$mollet, Crispy Malawi, Krazie G, Ace Dirty, Hayze Engola, Trappy Beats

[Intro: Crispy Malawi]
Yea
Mhahahaha
Brr Gang, gang, gang, gang
Gang, gang, gang, gang, gang
Hahahaha
Malawian
Aseh Trappy!
Yeah, Yea

[Chorus: Crispy Malawi]
Umaopa chani? (chani?)
Umaopa ndani? (Ndani?)
Umaopa Jah Jah olo umaopa Man? (Hmm)
Umakonda ndani?
Umakonda anzako olo umakonda ndani? (Hmm)
Ife timakonda money (money), nde gang yonse apa ndi
Ma millionaire ma millionaire
(Ndife) Ma billionaire ma billionaire yeah
Ma millionaire ma millionaire (aah)
Ma billionaire ma billionaire ha

[Verse: K1 $moillet]
Malo mowopa Jah Jah bwanji umaopa plain? (Ndege)
Malo mowopa mowa bwanji umaopa rain? (Rain)
Question mark? Zandidabwitsa (uh)
Now he's best believer after ndangomubamditsa
Kwa Jah Jah nachongetsa olo nditakwachitsa (yeah)
Kwa Jah Jah nakwanitsa olo nditakanikha (uh huh)
Game nditha Ku runner olo nditabanika
Sindingakhale broke nigga olo nditaphwanyika (haa)

[Verse 2: Crispy Malawi]
Chikhwaya cha Mangochi, millionaire mu bed sitter
Ndikamaliza mansion uzadziwadi ndine o hitter
Ati Spe "bwanji sumamuyankha kape uja pa Twitter"
Ndati "mwina fukwa Jah Jah nagolenga zau leader" (leader)
Ndili ndi G wopenga, ndi I want wafumbi
Kuyituluka hoes nthawi yamvula ndi ngumbi
Ndimawopa njala ndichisumphi
Sindingawope mkazi wachithako ndi chipumi
Ndi Chipumi you feel me? (No way)

[Verse 3: Hayze Engolah]
I've been on the ground for a long time
You know the rules you ain't eatin' osasonkha
Long nights in the stu osagona
We never get to hang with Spe's on the corners
Once the money counter go Brr, brr, brr every day
I'm a G, I go to sleep with all my mother fuckin' tapes
Flip the bag a hundred ways
If a nigga cross the line then we fund raising
Wangowona combination wangodziwa Ali safe
Akuyesa Pali space chonsecho Pali Spe
Dollar zingothoka zokha koma chonsecho ali phee
Ndungoflowa mwachikoka ondiponsa palibe (brr)

[Verse 4 : Krazie G]
All my life, all my life, I've been grindin'
All my life I've been own business mindin'
Most of time ndili ndi Ace ali ndi Phin
Ndili ndi Spe Ali ndi Gin, ndi K1 Ku 18
Two seater no denga, mfana opita Kazengwa
Ndango deleter ma number onse osabweletsa cheddar
Mfana oblowa Archaida ndimasowa amajeda
Mutu ma line utha kuyesa ndima cedar
Ukulenga ukuwona Ngati ukundi judger
Ukupenga Koma sunganmaizire ganja
Ndili mu street Ngati vendor ndi Hayze, Son wa Hender
Ma goon tumiza desenda nkublenda mafanzi ango surrender
Manja mwamba akuwaver tiku dripper Ngati mkaka
Verse iyi ndiya Mulaka Manjamo
(Mwamba!)
(Mwamba!) Manjamo
Clap clap if you ask me (Mwamba)
(Mwamba!) Dancehall daddy
(Mwamba!) (Hahaha)
Yeah
(Mwamba!)
(Mwamba!)

[Verse 5: Ace Dirty]
Okay
Ndimawopa nkhanza sindiwopa Panza (Ayi)
Ndimawopa AIDS sindiwopa X (Ayi)
Sindiwopa stress (no), sindiwopa flex (no)
Ndili top Ngati koka sindithoka Pepsi
Akufuna MO, ha Ngati 626
Pali Bros ndi Engola ballin' six to six
I just need two spliff (yea), one bottle of wine
Plus I need two chicks
Still spend old money, I don't need new licks (no)
Ndi chi chick cha chithako
I don't give two shits (chithako, chithako, chithako)
Yeah
Ndimakonda money (yeah), sindikonda nkhani (yeah)
Ndimakonza plan (yeah) kuwayenda pansi kuwaponda mapazi Ngati pa Mpani (pa Mpani)
Now you tell me who the man
I am mother brr hahaha

Altri artisti di